Mateyu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inde, adzakutengerani kwa abwanamkubwa ndi mafumu+ chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni+ kwa iwo ndi kwa anthu a mitundu ina. 2 Akorinto 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 kumenyedwa, kuponyedwa m’ndende,+ kukumana ndi zipolowe, kugwira ntchito mwakhama, kusagona tulo, ndi kukhala osadya.+
18 Inde, adzakutengerani kwa abwanamkubwa ndi mafumu+ chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni+ kwa iwo ndi kwa anthu a mitundu ina.
5 kumenyedwa, kuponyedwa m’ndende,+ kukumana ndi zipolowe, kugwira ntchito mwakhama, kusagona tulo, ndi kukhala osadya.+