Machitidwe 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Nthawi yomweyo amuna amene anafuna kumufufuza mwa kumuzunza aja anachoka n’kumusiya yekha. Nayenso mkulu wa asilikali uja anachita mantha atadziwa kuti ndi Mroma+ ndiponso kuti anamumanga.
29 Nthawi yomweyo amuna amene anafuna kumufufuza mwa kumuzunza aja anachoka n’kumusiya yekha. Nayenso mkulu wa asilikali uja anachita mantha atadziwa kuti ndi Mroma+ ndiponso kuti anamumanga.