Machitidwe 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti mwamphamvu, iye anawatsimikizira Ayuda poyera kuti anali olakwa, ndipo anasonyeza mwa Malemba+ kuti Yesu ndiyedi Khristu.+ Agalatiya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kalanga ine, Agalatiya opusa inu! Kodi ndani anakupotozani maganizo,+ inu amene munakhala ngati mwaona Yesu Khristu atapachikidwa pamtengo?+
28 Pakuti mwamphamvu, iye anawatsimikizira Ayuda poyera kuti anali olakwa, ndipo anasonyeza mwa Malemba+ kuti Yesu ndiyedi Khristu.+
3 Kalanga ine, Agalatiya opusa inu! Kodi ndani anakupotozani maganizo,+ inu amene munakhala ngati mwaona Yesu Khristu atapachikidwa pamtengo?+