Luka 22:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo mngelo wochokera kumwamba anaonekera kwa iye ndi kumulimbikitsa.+ Machitidwe 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+
11 Koma tsiku lomwelo usiku, Ambuye anaimirira pambali pake+ ndi kunena kuti: “Limba mtima!+ Pakuti wandichitira umboni mokwanira+ mu Yerusalemu, ndipo ukandichitiranso umboni ku Roma.”+