Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako anagona pansi mpaka tulo tinam’peza pansi pa kamtengo kaja.+ Tsopano kunabwera mngelo+ amene anamukhudza,+ n’kumuuza kuti: “Dzuka udye.”

  • Yesaya 49:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova wanena kuti: “Pa nthawi yapadera yosonyeza kukoma mtima kwanga, ndinakuyankha.+ M’tsiku la chipulumutso, ndinakuthandiza.+ Ndinakuteteza kuti ndikupereke ngati pangano kwa anthu,+ kuti ndikonzenso dzikolo,+ kuti anthu ayambirenso kukhala m’cholowa chawo chimene chinali bwinja,+

  • Danieli 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno wamaonekedwe ofanana ndi munthu wochokera kufumbi uja anandikhudza ndi kundilimbikitsa.+

  • Mateyu 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Mdyerekezi uja anamusiya,+ ndipo kunabwera angelo ndi kuyamba kum’tumikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena