Aroma 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikufuna kukudziwitsani za mlongo wathu Febe, amene akutumikira+ mumpingo wa ku Kenkereya.+