Aroma 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndimamupempha kuti ngati n’kotheka mwa chifuniro+ chake, ulendo uno wokha ndibwere kwanuko. 1 Akorinto 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ndifika kwanuko posachedwapa, Yehova akalola,+ ndipo sindidzafuna kumva mawu a odzitukumulawo, koma ndidzafuna ndione mphamvu yawo. Yakobo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+
19 Koma ndifika kwanuko posachedwapa, Yehova akalola,+ ndipo sindidzafuna kumva mawu a odzitukumulawo, koma ndidzafuna ndione mphamvu yawo.
15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+