Machitidwe 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja Aroma 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 kuti ndikadzafika kwa inu ndi chisangalalo mwa kufuna kwa Mulungu, tidzalimbikitsidwe pamodzi.+ Yakobo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+
21 M’malomwake, anatsanzikana+ nawo ndi kuwauza kuti: “Yehova akalola ndidzabweranso kudzakuonani.”+ Choncho ananyamuka ku Efeso ulendo wa panyanja
15 M’malomwake, muyenera kunena kuti: “Yehova akalola,+ tikhala ndi moyo, ndi kuchita zakutizakuti.”+