Afilipi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikuyesetsa kuchita zimenezi mpaka nditapeza+ mphoto+ ya chiitano cha Mulungu chopita kumwamba,+ chodzera mwa Khristu Yesu. 1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna. Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
14 Ndikuyesetsa kuchita zimenezi mpaka nditapeza+ mphoto+ ya chiitano cha Mulungu chopita kumwamba,+ chodzera mwa Khristu Yesu.
12 n’cholinga choti mupitirize kuyenda+ m’njira imene Mulungu, amene akukuitanani+ ku ufumu+ wake ndi ulemerero, amafuna.
3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+