11 Namani atamva zimenezi anapsa mtima+ n’kunyamuka kuti azipita, ndipo anati: “Ine ndinati,+ ‘Abwera kudzaima pafupi ndi ine n’kuitana dzina la Yehova Mulungu wake. Kenako ayendetsa dzanja lake uku ndi uku pamwamba pa malo amatendawo n’kundichiritsa khate langali.’