-
Genesis 17:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Tsopano dzina lako silikhalanso Abulamu, m’malo mwake likhala Abulahamu, chifukwa ndidzakupangitsa kukhala tate wa mitundu yambiri.
-