Maliko 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungathe kumwa zimene ine ndikumwa, kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa nawo?”+ 1 Akorinto 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Apo ayi, kodi amene akubatizidwa kuti akhale akufa adzatani?+ Ngati akufa sadzauka,+ n’chifukwa chiyani anthuwo akubatizidwa+ kuti akhale akufa?
38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungathe kumwa zimene ine ndikumwa, kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa nawo?”+
29 Apo ayi, kodi amene akubatizidwa kuti akhale akufa adzatani?+ Ngati akufa sadzauka,+ n’chifukwa chiyani anthuwo akubatizidwa+ kuti akhale akufa?