1 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mulungu anaukitsa Ambuye+ kwa akufa+ ndipo adzaukitsanso ife mwa mphamvu yake.+ 2 Timoteyo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawu awa ndi oona,+ akuti: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+
11 Mawu awa ndi oona,+ akuti: Ndithudi, ngati tinafa naye limodzi, tidzakhalanso ndi moyo limodzi naye.+