1 Akorinto 15:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndi mmenenso zilili ndi kuuka kwa akufa.+ Thupi limafesedwa lili lokhoza kuwonongeka, limaukitsidwa losakhoza kuwonongeka.+ 1 Akorinto 15:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo. Aefeso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo anatikweza+ pamodzi, ndi kutikhazika pamodzi m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu Yesu.
42 Ndi mmenenso zilili ndi kuuka kwa akufa.+ Thupi limafesedwa lili lokhoza kuwonongeka, limaukitsidwa losakhoza kuwonongeka.+
49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo.