Machitidwe 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa kwa akufa, osayembekezera kubwereranso kuthupi limene lingathe kuvunda, anaitchula motere, ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu kukoma mtima kwanga kosatha ndi kokhulupirika, kumene ndinasonyeza Davide.’+ 1 Akorinto 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Komabe, Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ n’kukhala chipatso choyambirira+ cha amene akugona mu imfa.+
34 Ndipo mfundo yakuti iye anamuukitsa kwa akufa, osayembekezera kubwereranso kuthupi limene lingathe kuvunda, anaitchula motere, ‘Ine ndidzakusonyezani anthu inu kukoma mtima kwanga kosatha ndi kokhulupirika, kumene ndinasonyeza Davide.’+
20 Komabe, Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ n’kukhala chipatso choyambirira+ cha amene akugona mu imfa.+