Salimo 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti zolakwa zanga ndikuzidziwa bwino,+Ndipo tchimo langa lili pamaso panga nthawi zonse.+ Luka 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma wokhometsa msonkho uja, ataima chapatali ndithu, sanafune ngakhale kukweza maso ake kumwamba. Anali kungodziguguda pachifuwa+ ndi kunena kuti, ‘Mulungu wanga, ndikomereni mtima munthu wochimwa ine.’+
13 Koma wokhometsa msonkho uja, ataima chapatali ndithu, sanafune ngakhale kukweza maso ake kumwamba. Anali kungodziguguda pachifuwa+ ndi kunena kuti, ‘Mulungu wanga, ndikomereni mtima munthu wochimwa ine.’+