Yohane 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+ 1 Akorinto 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mwa mzimu+ wake, Mulungu anaululira+ ifeyo zinthu zimenezi, chifukwa mzimu+ umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama+ za Mulungu. Tito 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anatikhuthulira mzimu umenewu kudzera mwa Yesu Khristu Mpulumutsi wathu,+
17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+
10 Pakuti mwa mzimu+ wake, Mulungu anaululira+ ifeyo zinthu zimenezi, chifukwa mzimu+ umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama+ za Mulungu.