Yohane 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo,+ mnofu n’ngopanda phindu. Mawu amene ndakuuzaniwa ndiwo mzimu+ ndiponso ndiwo moyo.+ Yohane 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+ 1 Akorinto 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mwa mzimu+ wake, Mulungu anaululira+ ifeyo zinthu zimenezi, chifukwa mzimu+ umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama+ za Mulungu. 1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu. 2 Timoteyo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+
63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo,+ mnofu n’ngopanda phindu. Mawu amene ndakuuzaniwa ndiwo mzimu+ ndiponso ndiwo moyo.+
17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+
10 Pakuti mwa mzimu+ wake, Mulungu anaululira+ ifeyo zinthu zimenezi, chifukwa mzimu+ umafufuza zinthu zonse, ngakhale zinthu zozama+ za Mulungu.
14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+