Deuteronomo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Silili kumwamba kuti unene kuti, ‘Ndani adzakwera kumwamba ndi kukatitengera lamulolo kuti ife tilimve ndi kulitsatira?’+
12 Silili kumwamba kuti unene kuti, ‘Ndani adzakwera kumwamba ndi kukatitengera lamulolo kuti ife tilimve ndi kulitsatira?’+