2 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano, popeza tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi umene anaunena kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, chotero ndinalankhula,”+ ifenso tili ndi chikhulupiriro, chotero tikulankhula, Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
13 Tsopano, popeza tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi umene anaunena kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, chotero ndinalankhula,”+ ifenso tili ndi chikhulupiriro, chotero tikulankhula,
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+