Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ Miyambo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anayala maziko a dziko lapansi mwanzeru.+ Anakhazikitsa kumwamba mozindikira.+