Miyambo 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamene anali kukonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+ Pamene anakhazikitsa lamulo lakuti pamwamba pa madzi akuya pazioneka pozungulira,+ Yeremiya 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru+ zake anakhazikitsa dziko+ limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+
27 Pamene anali kukonza kumwamba, ine ndinali pomwepo.+ Pamene anakhazikitsa lamulo lakuti pamwamba pa madzi akuya pazioneka pozungulira,+
15 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru+ zake anakhazikitsa dziko+ limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+