6 Tsopano abale, zinthu zimenezi ndazinena monga zochitika kwa ine mwini ndi Apolo+ kuti inuyo mupindule, kuti muphunzire kwa ife lamulo ili lakuti: “Musapitirire zinthu zolembedwa,”+ kuti aliyense wa inu asadzitukumule+ pokonda munthu wina n’kudana ndi wina.+