Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti sipadzalephera kukhala wosauka m’dziko lako.+ N’chifukwa chake ndikukulamula kuti, ‘Uzikhala wowolowa manja kwa m’bale wako wovutika ndi wosauka m’dziko lanu.’+

  • Miyambo 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Munthu wopatsa mowolowa manja adzalandira mphoto,+ ndipo wothirira ena mosaumira nayenso adzathiriridwa mosaumira.+

  • 2 Akorinto 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamene iwo anali kuyesedwa kwambiri chifukwa cha mavuto, anali achimwemwe kwambiri ndiponso anasonyeza kuwolowa manja kwakukulu, ndipo anachita zimenezi ngakhale kuti anali pa umphawi wadzaoneni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena