1 Akorinto 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chikondi+ n’choleza mtima+ ndiponso n’chokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama,+ sichidzikuza,+
4 Chikondi+ n’choleza mtima+ ndiponso n’chokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama,+ sichidzikuza,+