Luka 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni,+ kuti munthu amene wakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Pamenepo udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+ Yohane 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho ngati ine, wokhala Ambuye ndi Mphunzitsi, ndasambitsa mapazi anu,+ inunso muyenera kusambitsana mapazi.+ Aefeso 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muziyenda modzichepetsa nthawi zonse,+ mofatsa, moleza mtima,+ ndiponso mololerana m’chikondi.+ Afilipi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+
10 Koma ukaitanidwa, pita ndipo ukakhale kumapeto kwenikweni,+ kuti munthu amene wakuitana uja akafika adzakuuze kuti, ‘Bwanawe, khala pamalo aulemuwa.’ Pamenepo udzalemekezeka pamaso pa alendo anzako onse.+
14 Choncho ngati ine, wokhala Ambuye ndi Mphunzitsi, ndasambitsa mapazi anu,+ inunso muyenera kusambitsana mapazi.+
3 Musachite chilichonse ndi mtima wokonda mikangano+ kapena wodzikuza,+ koma modzichepetsa, ndi kuona ena kukhala okuposani.+