1 Petulo 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pakuti zili bwino ngati wina, chifukwa cha chikumbumtima chake kwa Mulungu, akupirira zowawa ndi kuvutika popanda mlandu.+ 1 Petulo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+
19 Pakuti zili bwino ngati wina, chifukwa cha chikumbumtima chake kwa Mulungu, akupirira zowawa ndi kuvutika popanda mlandu.+
16 Khalani ndi chikumbumtima chabwino,+ kuti ngakhale azikunenerani zoipa ndi kulankhula monyoza za khalidwe lanu labwino monga otsatira Khristu, adzachite manyazi.+