Aroma 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero pali chifukwa chabwino chakuti anthu inu mukhalire ogonjera, osati chabe chifukwa choopa mkwiyo umenewo, komanso chifukwa cha chikumbumtima chanu.+
5 Chotero pali chifukwa chabwino chakuti anthu inu mukhalire ogonjera, osati chabe chifukwa choopa mkwiyo umenewo, komanso chifukwa cha chikumbumtima chanu.+