1 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzitsanzira ine, monga mmene inenso ndimatsanzirira Khristu.+ Agalatiya 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti nonsenu amene munabatizidwa mwa Khristu+ mwavala Khristu.+ Aefeso 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.
24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.