Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 11:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Choncho ngati inu, ngakhale kuti ndinu oipa, mumadziwa kupatsa ana anu+ mphatso zabwino, kuli bwanji Atate wakumwamba! Ndithudi iye adzapereka mowolowa manja mzimu woyera+ kwa amene akum’pempha.”

  • Aefeso 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi,+ omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu.+ Kudzeranso mwa iye, mutakhulupirira munaikidwa chidindo+ cha mzimu woyera wolonjezedwawo,+

  • 1 Timoteyo 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndithudi, chinsinsi chopatulikachi+ chokhudza kukhala odzipereka kwa Mulungu n’chachikulu ndithu: ‘Iye anaonekera ngati munthu,+ anaonedwa kuti ndi wolungama pamene anali mzimu,+ anaonekera kwa angelo,+ analalikidwa kwa mitundu ya anthu,+ anthu padziko lapansi anamukhulupirira,+ ndiponso analandiridwa kumwamba mu ulemerero.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena