1 Akorinto 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye. Akolose 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mundiperekere moni kwa abale a ku Laodikaya ndi kwa Numfa ndi mpingo umene umasonkhana panyumba pake.+ Filimoni 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mlongo wathu Apiya ndiponso msilikali mnzathu+ Arikipo,+ ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwako:+
19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye.
15 Mundiperekere moni kwa abale a ku Laodikaya ndi kwa Numfa ndi mpingo umene umasonkhana panyumba pake.+
2 mlongo wathu Apiya ndiponso msilikali mnzathu+ Arikipo,+ ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwako:+