5 Ndikuperekanso moni ku mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo.+ Moni kwa wokondedwa wanga Epeneto, amene ndi chipatso choyambirira+ cha Khristu mu Asia.
19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni.+ Akula ndi Purisika, pamodzi ndi mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa inu nonse, mwa Ambuye.