Aroma 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikanakonda kuti ineyo ndichotsedwe kwa Khristu monga wotembereredwa m’malo mwa abale anga,+ amene ali anthu a mtundu wanga.+ Aroma 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ ndi akaidi anzanga.+ Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana+ ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ine.
3 Ndikanakonda kuti ineyo ndichotsedwe kwa Khristu monga wotembereredwa m’malo mwa abale anga,+ amene ali anthu a mtundu wanga.+
7 Moni kwa Anduroniko ndi Yuniya, omwe ndi achibale anga+ ndi akaidi anzanga.+ Amenewa ndi amuna odziwika kwambiri kwa atumwi ndiponso akhala ogwirizana+ ndi Khristu kwa nthawi yaitali kuposa ine.