Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mwamuna ameneyu analangizidwa njira ya Yehova ndi mawu a pakamwa. Ndiyeno popeza kuti anali wodzipereka kwambiri chifukwa chakuti anali ndi mzimu woyera,+ anali kulankhula ndi kuphunzitsa molondola za Yesu. Koma anali kudziwa za ubatizo+ wa Yohane wokha basi.

  • Machitidwe 18:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Pakuti mwamphamvu, iye anawatsimikizira Ayuda poyera kuti anali olakwa, ndipo anasonyeza mwa Malemba+ kuti Yesu ndiyedi Khristu.+

  • Machitidwe 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena