Ekisodo 34:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aroni ndi ana onse a Isiraeli ataona Mose, anaona kuti nkhope yake ikuwala, ndipo anaopa kumuyandikira.+
30 Aroni ndi ana onse a Isiraeli ataona Mose, anaona kuti nkhope yake ikuwala, ndipo anaopa kumuyandikira.+