Ekisodo 34:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aroni ndi Aisiraeli onse ataona Mose, anaona kuti nkhope yake ikuwala ndipo anaopa kumuyandikira.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:30 Nsanja ya Olonda,3/15/1990, tsa. 7
30 Aroni ndi Aisiraeli onse ataona Mose, anaona kuti nkhope yake ikuwala ndipo anaopa kumuyandikira.+