Aroma 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero, mzimu wa amene anaukitsa Yesu kwa akufa ukakhala mwa inu, iye amene anaukitsa Khristu Yesu kwa akufa+ adzachititsanso matupi anu otha kufawo kukhala ndi moyo+ mwa mzimu wake umene ukukhala mwa inu. 1 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Mulungu anaukitsa Ambuye+ kwa akufa+ ndipo adzaukitsanso ife mwa mphamvu yake.+
11 Chotero, mzimu wa amene anaukitsa Yesu kwa akufa ukakhala mwa inu, iye amene anaukitsa Khristu Yesu kwa akufa+ adzachititsanso matupi anu otha kufawo kukhala ndi moyo+ mwa mzimu wake umene ukukhala mwa inu.