2 Akorinto 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati ndingafune kudzitamandira, si kuti ndikhala wodzikweza,+ chifukwa ndikhala ndikunena choonadi. Koma sindikudzitamandira, chifukwa ndikufuna kuti inuyo mundiyamikire pa zinthu zokhazo zimene mukuona kapena kumva kwa ine.
6 Ngati ndingafune kudzitamandira, si kuti ndikhala wodzikweza,+ chifukwa ndikhala ndikunena choonadi. Koma sindikudzitamandira, chifukwa ndikufuna kuti inuyo mundiyamikire pa zinthu zokhazo zimene mukuona kapena kumva kwa ine.