2 Akorinto 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi pamene sindili kumeneko, kuti ndikadzakhalako ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu,+ chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu kuti ndizikulimbikitsani,+ osati kukufooketsani. Aheberi 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+
10 N’chifukwa chake ndikulemba zinthu zimenezi pamene sindili kumeneko, kuti ndikadzakhalako ndisadzagwiritse ntchito ulamuliro wanga mwamphamvu,+ chifukwa Ambuye anandipatsa ulamulirowu kuti ndizikulimbikitsani,+ osati kukufooketsani.
17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+