Luka 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera+ udzafika pa iwe, ndipo mphamvu ya Wam’mwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechinso, wodzabadwayo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+ Machitidwe 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yomweyo anayamba kulalikira za Yesu m’masunagoge,+ kuti Ameneyu ndiye Mwana wa Mulungu.
35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera+ udzafika pa iwe, ndipo mphamvu ya Wam’mwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechinso, wodzabadwayo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+