2 Akorinto 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndikuona kuti sindikuchepa+ mwanjira ina iliyonse kwa atumwi anu apamwambawo.+ Chivumbulutso 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ‘Ndikudziwa ntchito zako,+ khama lako, ndi kupirira kwako, ndiponso kuti sungalekelere anthu oipa. Iwe unayesanso+ anthu amene amadzitcha atumwi+ pamene sanali atumwi, ndipo unapeza kuti ndi onama.
2 ‘Ndikudziwa ntchito zako,+ khama lako, ndi kupirira kwako, ndiponso kuti sungalekelere anthu oipa. Iwe unayesanso+ anthu amene amadzitcha atumwi+ pamene sanali atumwi, ndipo unapeza kuti ndi onama.