Luka 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Simoni, Simoni! Ndithu Satana+ akufuna anthu inu, kuti akupeteni ngati tirigu.+ Aefeso 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 chifukwa sitikulimbana+ ndi anthu athupi la magazi ndi nyama ayi, koma ndi maboma,+ maulamuliro,+ olamulira dziko+ a mdimawu, ndi makamu a mizimu yoipa+ m’malo akumwamba. 2 Timoteyo 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso kuti mwina nzeru zawo zingabwereremo kuti awonjoke mumsampha+ wa Mdyerekezi, poona kuti wawagwira amoyo+ pofuna kukwaniritsa cholinga chake.
12 chifukwa sitikulimbana+ ndi anthu athupi la magazi ndi nyama ayi, koma ndi maboma,+ maulamuliro,+ olamulira dziko+ a mdimawu, ndi makamu a mizimu yoipa+ m’malo akumwamba.
26 Komanso kuti mwina nzeru zawo zingabwereremo kuti awonjoke mumsampha+ wa Mdyerekezi, poona kuti wawagwira amoyo+ pofuna kukwaniritsa cholinga chake.