Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 54:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 “Iwe mkazi wosabereka amene sunaberekepo mwana,+ fuula mokondwa!+ Iwe amene sunamvepo zowawa za pobereka,+ kondwera! Fuula mokondwa! Kuwa ndi chisangalalo, pakuti ana a mkazi wosiyidwa ndi ambiri kuposa ana a mkazi yemwe ali ndi mwamuna,”+ watero Yehova.

  • Aroma 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero, ngati tili ana, tilinso olandira cholowa: Olandira cholowa a Mulungu, komanso olandira cholowa anzake+ a Khristu, malinga ngati tivutika+ naye limodzi kuti tikalandire ulemerero limodzi ndi iye.+

  • Aroma 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiponso si onse amene ali ana chifukwa chongokhala mbewu ya Abulahamu.+ Koma Malemba amati, “Amene adzatchedwa ‘mbewu yako’ adzachokera mwa Isaki.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena