Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 12:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “Musaope,+ kagulu ka nkhosa+ inu, chifukwa Atate wanu wavomereza kukupatsani ufumu.+

  • Machitidwe 26:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ukatsegule maso awo,+ kuwachotsa mu mdima+ ndi kuwatembenuzira ku kuwala.+ Kuwachotsa m’manja mwa Satana+ ndi kuwatembenuzira kwa Mulungu, kuti machimo awo akhululukidwe+ ndi kukalandira cholowa+ pamodzi ndi oyeretsedwa,+ mwa chikhulupiriro chawo mwa ine.’

  • Agalatiya 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+

  • Chivumbulutso 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena