1 Akorinto 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mdulidwe+ sutanthauza kalikonse, ndipo kusadulidwa+ sikutanthauza kanthu, koma kusunga malamulo a Mulungu ndiko kofunika.+ Agalatiya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo ngakhale Tito,+ amene ndinali naye limodzi, sanafunikire kudulidwa,+ ngakhale kuti iye ndi Mgiriki. Agalatiya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti kudulidwa kapena kusadulidwa si kanthu,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+ Akolose 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mukatero, sipadzakhala Mgiriki kapena Myuda, kudulidwa kapena kusadulidwa, mlendo, Msukuti, kapolo, kapena mfulu,+ koma Khristu ndiye zinthu zonse ndipo ali mwa onse.+
19 Mdulidwe+ sutanthauza kalikonse, ndipo kusadulidwa+ sikutanthauza kanthu, koma kusunga malamulo a Mulungu ndiko kofunika.+
3 Ndipo ngakhale Tito,+ amene ndinali naye limodzi, sanafunikire kudulidwa,+ ngakhale kuti iye ndi Mgiriki.
15 Pakuti kudulidwa kapena kusadulidwa si kanthu,+ koma chofunika ndi kukhala wolengedwa mwatsopano.+
11 Mukatero, sipadzakhala Mgiriki kapena Myuda, kudulidwa kapena kusadulidwa, mlendo, Msukuti, kapolo, kapena mfulu,+ koma Khristu ndiye zinthu zonse ndipo ali mwa onse.+