Machitidwe 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Paulo anaonetsa kuti akufuna kumutenga pa ulendo wake. Chotero anamutenga ndi kum’dula+ chifukwa cha Ayuda amene anali kumeneko, pakuti onse anali kudziwa kuti bambo ake ndi Mgiriki.
3 Paulo anaonetsa kuti akufuna kumutenga pa ulendo wake. Chotero anamutenga ndi kum’dula+ chifukwa cha Ayuda amene anali kumeneko, pakuti onse anali kudziwa kuti bambo ake ndi Mgiriki.