1 Akorinto 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+ Akolose 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye ndiyenso mutu wa thupilo, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndiye chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba+ pa zinthu zonse.
3 Koma ndikufuna mudziwe kuti mutu wa mwamuna aliyense ndi Khristu.+ Mutu wa mkazi ndi mwamuna,+ ndipo mutu wa Khristu ndiye Mulungu.+
18 Iye ndiyenso mutu wa thupilo, lomwe ndi mpingo.+ Iye ndiye chiyambi, woyamba kubadwa kuchokera kwa akufa,+ kuti adzakhale woyamba+ pa zinthu zonse.