1 Timoteyo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mawu awa ndi oona.+ Ngati munthu aliyense akuyesetsa kuti akhale woyang’anira,+ akufuna ntchito yabwino. 1 Timoteyo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nawonso atumiki othandiza+ akhale opanda chibwana, osanena pawiri, osakonda kumwa vinyo wambiri, ndiponso osakonda kupeza phindu mwachinyengo.+
3 Mawu awa ndi oona.+ Ngati munthu aliyense akuyesetsa kuti akhale woyang’anira,+ akufuna ntchito yabwino.
8Â Nawonso atumiki othandiza+ akhale opanda chibwana, osanena pawiri, osakonda kumwa vinyo wambiri, ndiponso osakonda kupeza phindu mwachinyengo.+