Yesaya 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanditsegula khutu ndipo ineyo sindinapanduke.+ Sindinatembenukire kwina.+ Yohane 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chimene Atate amandikondera n’chakuti,+ ndikupereka moyo wanga+ kuti ndikaulandirenso. Aheberi 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti anali Mwana wa Mulungu, anaphunzira kumvera chifukwa cha mavuto amene anakumana nawo.+
5 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanditsegula khutu ndipo ineyo sindinapanduke.+ Sindinatembenukire kwina.+
8 Ngakhale kuti anali Mwana wa Mulungu, anaphunzira kumvera chifukwa cha mavuto amene anakumana nawo.+