Aefeso 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 umene ndi thupi lake.+ Mpingowo ndi wodzaza+ ndi iye, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.+ Akolose 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zili motero chifukwa kunamukomera Mulungu kuti zinthu zonse+ zikhale mwa mwana wakeyo ndipo zidzazemo bwino.
19 Zili motero chifukwa kunamukomera Mulungu kuti zinthu zonse+ zikhale mwa mwana wakeyo ndipo zidzazemo bwino.